ANATCHEZERA

ANATCHEZERA

ANatchereza

Sakufuna kukaonekera Gogo Natchereza, Mnyamata wina adandifunsira chibwenzi ndi cholinga choti tidzakwatirane. Padakali pano padutsa zaka zinayi tili paubwenzi, koma...

Anatchezera

Sakufuna kukaonekera Gogo Natchereza, Mnyamata wina adandifunsira chibwenzi ndi cholinga choti tidzakwatirane. Padakali pano padutsa zaka zinayi tili paubwenzi, koma...

anatchezera

Akundidabwitsa Anatchereza, Ndili pa chibwenzi ndi mwamuna wina. Chomwe chimandidabwitsa n’choti nthawi zonse ndikamuimbira foni usiku samayankha. Ndikamufunsa amati idali...

Anatchereza

Ndikufuna kuchoka Zikomo Anatchereza, Ndidabwera kutauni kudzafuna ntchito ndipo ndidasiya mkazi wanga kumudzi. Ntchito ndidaipeza koma abale amene ndimakhala m’nyumba...

Anatchezera

Ukuchita njomba Gogo Natcheteza, Ndine mtsikana wa zaka 25 ndipo ndakhala pa chibwenzi ndi mnyamata wina kwa zaka zinayi. Mnyamatayu...

Anatchezera

Akundifunanso Anatchereza, Telemu yotsiriza ya Fomu 3 ndidapalana ubwenzi ndi mtsikana wina pasukulu yathu ku Mulanje. Koma tikuyandikira kulemba mayeso...

ANATCHEZERA

Adandichotsa ntchito Zikomo Gogo Ndakhala ndikugwira ntchito kwa bwana wina mumzinda wa Blantyre kwa zaka 4. Masiku apitawa ndidaapempha holide...

Anatchereza

Mkazi wanga koma mkonono Agogo, Langa ndi dandaulo pa mkazi wanga wokondeka. Iyetu mwano alibe ndiponso ntchito amagwira molimbika. Abale...

Anatchezera

Akunyengana ndi mnzanga Zikomo Anatchereza, Ndakhala pabanja zaka 7 ndipo tilinso ndi mwana wa zaka 7. Tsiku lina mwanayo adathyoka...

Anatchezera

ANATCHEREZA Akundikakamira Ndili ndi mkazi yemwe ndili naye mwana mmodzi. Vuto lake ndi limodzi: amakhalira kunyoza makolo ndi abale anga....

Anatchezera

Ndikufuna sukulu Zikomo Anatchereza, Ndine msungwana wa zaka 19. Sindidakwatiwepo, ngakhale sukulu ndidaisiyira Fomu 1 zaka zutatu zapitazo. Sukuluyo ndidasiya...

Anatchezera

Za chikondi ndi chibwenzi Agogo, Kodi chibwenzi ndi chikondi ndi zosiyana bwanji? Mwina funso limeneli likhoza kuoneka ngati lopanda nzeru...

Anatchereza

Wokondedwa Anatchereza, Zikomo chifukwa cha malangizo amene mukumapereka. Thandizeni. Ndili ndi mkazi yemwe ndakhala naye kwa nthawi ndithu. Iye adapezeka...

Anatchezera

Ndimufunsirebe? Ndine mnyamata wa mu Lilongwe ndipo ndidagwa m’chikondi ndi msungwana wina. Ndakhala ndikuponya mawu kwa iye koma iyeyo amayankha...

Anachezera

Zidatheka! Zikomo Anatchereza, Ndafuna ndikuthokozeni kwambiri chifukwa cha malangizo anu. Pano tidamanga banja ndi mtsikana wa ku Machinga uja ndipo...

Anatchezera

Chikondi amatero? Agogo, Ndine mtsikana wa zaka 20 ndipo ndili kukoleji. Ndili ndi chibwenzi chomwe tidagwirizana kuti tidzamange banja mtsogolo...

Anatchezera

Akundimana Anatchereza, Ndakhala pabanja ndi mkazi wanga kuyambira mu 2011. Poyamba zonse zimayenda koma masiku ano ndikamufuna masiku ambiri amanena...

Anatchezera

Ndazunguzika Agogo, Ndine mtsikana wa zaka 18 ndipo ndinazunguzika mutu chaka chatha pomwe ndinapezeka ndi kachilombo ka HIVkoma sindinagonepo ndi...

Page 1 of 3 1 2 3

Opinions and Columns