ANATCHEZERA

ANATCHEZERA

Anatchezera

Akufuna mwana Zikomo Gogo, Banja ndi mwamuna wanga lidatha mu 2011. Ndidapeza mwamuna wina yemwe timamvana ndipo tidakayezetsa komwe adatipeza...

Anatchezera

Anzanga sakundifunsira Ndine mtsikana wa zaka 20, vuto ndili nalo ndi loti sindikufunsiridwa ndi anyamata amsinkhu wanga koma okwatira okhaokha....

Anatchezera

Sakuthandiza Agogo, Ndine mtsikana wa zaka 21 ndipo ndili ndi mwana mmodzi. Amuna anga adandisiya ataona kuti ndili ndi pathupi...

ANATCHEZERA

Wamkulu ndine Zikomo agogo, Ndili ndi chibwenzi koma timasiyana ndi chaka chimodzi, wamkulu ndineyo. Kodi tingathe kukwatirana? Iyeyu akufunitsitsa atandikwatira...

Anatchezera

Sakufuna kukayezetsa Anatchereza, Ndakhala ndili pachibwenzi ndi mtsikana wina kwa chaka chimodzi ndipo timakondana kwambiri. Ndine Mkhristu ndipo ndikhulupirira kuti...

Anatchezera

Ndisathandize mwana wanga? Anatchereza Ine ndi mkazi wanga tidalekana titakhala pabanja zaka ziwiri. Mkaziyu ndidakukwatira titachimwitsana pasukulu ine ndili Fomu...

Anatchezera

Sagona m’nyumba Anatchereza, Ndili ndi zaka 20 ndipo amuna anga sagona m’nyumba ndiye chonde, ndithandizeni. Akuti ndikawauza ankhonswe banja langa...

Anatchezera

Nditani Anatchereza? Agogo, Ndine mtsikana wa zaka 20 ndipo ndili ku koleji. Ndili ndi chibwenzi chomwe tidagwirizana kuti tidzamange banja...

Anatchezera

Ndimamukonda Agogo, Ndinali pachibwenzi ndi mkazi wina ndipo zaka ziwiri zatha pomwe tinasiyana. Pano ali ndi mwana yemwe wabereka mwezi...

anatchezera

Amandimenya Zikomo gogo, Ndine mtsikana wa zaka 20 ndipo ndili pachibwenzi ndi mwamuna wa zaka 25. Tili ndi mwana mmodzi...

Anatchezera

Ndazunguzika Agogo, Ndine mtsikana wa zaka 18 ndipo ndinazunguzika mutu chaka chatha pomwe ndinapezeka ndi kachilombo ka HIVkoma sindinagonepo ndi...

Anatchezera

Sakuyankhanso foni Zikomo, Ndine mtsikana wa zaka 19 ndipo ndidapeza bwenzi langa mu 2012. Poyamba ankalimbikira kuti andikwatire chaka chomwecho...

Anatchezera

Amandikakamirabe Agogo, Ndine mtsikana wa zaka 19 zakubadwa, vuto langa ndi lakuti pali mnyamata wina wake amene amandifuna koma ineyo...

Anatchezera

  Akumandiipitsa Zikomo agogo, Ndili ndi chibwenzi ndipo makolo akudziwa ngakhale kuti ndi mwamphekesera chabe. Nthawi ina bambo ake (osati...

ANATCHEZERA

Sapereka chithandizo Agogo, Ndine mtsikana wa zaka 21 ndipo ndili ndi mwana mmodzi. Amuna anga adandisiya ataona kuti ndili ndi...

Anatchezera

Sakundilipira Zikomo gogo, Ndakhala ndikugwira ntchito kukampani ya alonda ina kwa miyezi 11 popanda masiku opuma. Mwezi ulionse amatidula K500...

Anatchezera

Sakuthandiza mwana Agogo, Ndine mtsikana wa zaka 19 ndipo ndili ndi mwana mmodzi. Ndidali pabanja koma litatha bambowo samatumiza chithandizo...

Anatchezera

Sitinakumanepo Anatchereza, Ndili ndi mkazi amene ndidamufunsira pafoni koma sitinaonanepo. Timangoimbirana foni basi koma amandiuza kuti amandikonda kwambiri. Ndimukhululupirire?  ...

ANATCHEZERA

Nditenge uti? Anatchereza, Munthune ndili ndi zibwenzi ziwiri. Zonsezi zidayamba chaka chimodzi panopa zatha zaka zitatu ndipo onsewa ndimawakonda chimodzimodzi...

Page 2 of 3 1 2 3

Opinions and Columns