ANATCHEZERA

ANATCHEZERA

Anatchezera

  Kwawo sindidziwako Agogo, Ndinapeza mwamuna kudzera patsamba lino ndipo ndikuyamika chifukwa chondithandiza. Komano vuto langa ndi loti amakana kuti...

Anatchezera

Akumandiipitsa Zikomo agogo, Ndili ndi chibwenzi ndipo makolo akudziwa ngakhale kuti ndi mwamphekesera chabe. Nthawi ina bambo ake (osati omubereka)...

Anatchezera

Sabata zingapo zapitazi, takhala tikulengeza kuti patsamba lino tizikupatsirani Anatchereza ndi malangizo pamavuto amene mumakumana nawo. Mavutowa akhoza kukhala a...

Anatchezera

Sakundikwatira Agogo, Ndithandizeni. Ndili paubwenzi ndi mwamuna yemwe adakwatirapo koma banja lake lidatha ndi mkaziyo ndipo kuli mwana mmodzi. Inenso...

ANATCHEZERA

Mkazi wanga asabwere? Anatchereza, Ndili ndi zaka 25 ndipo ndili pantchito yokhalira pomwepo. Ndine wokwatira ndipo ndili mwana mmodzi. Abwana...

anatchezera

Akuti tibwererane Anatchereza, Ndinali pambanja ndi mwamuna wa ku Nsanje ndipo ndili naye mwana mmodzi. Koma ndikati tiyeni tikaone kwanu...

Anatchezera

Banja lavuta Zikomo Anatchereza, Ndine mayi wa zaka 30 ndipo ndili ndi ana atatu. Kumbuyo kunseku timakhala bwinobwino ngakhale ndimamva...

Anatchezera

Wamboni, ine Msilamu Zikomo Anatchereza, Ndinagwa m’chikondi ndi mtsikana wa Mboni za Yehova mpaka ndinamuchimwitsa moti ndikunena pano kuli mwana...

ANATCHEZERA

Sitinakumanepo Anatchereza, Ine dangwa m’chikondi ndi munthu woti sindinakumanepo naye. Ndili ndi zaka 23 koma iye ndikamufunsa zaka zake samandiuza....

Page 3 of 3 1 2 3
ADVERTISEMENT

Opinions and Columns