Kasambara: Akhazikitsa chimbale mwezi uno
Martha Kasambala ndi woimba nyimbo zauzimu ndipo amakhala ku Mzuzu. Iye ali ndi zimbale ziwiri ndipo mu December muno akuti...
Martha Kasambala ndi woimba nyimbo zauzimu ndipo amakhala ku Mzuzu. Iye ali ndi zimbale ziwiri ndipo mu December muno akuti...
Police in Kasungu recently elected a station executive committee (SEC) during a meeting held at Kasungu Community Hall. The...
Martha Kasambara ndi woimba nyimbo za uzimu wokhala ku Mzuzu. Iye ali ndi zimbale ziwiri ndipo mu December chaka chino...
Kubangula ndi kulira mokweza kukumveka m’zipatala za m’dziko muno pomwe boma lachepetsa ndalama zopita kuntchito za chipatala potsatira mavuto a...
Bwalo lamilandu mumzinda wa Mzuzu lagamula Mulolo Nkhata wa zaka 18 kukakhala kundende zaka 18 atamupeza wolakwa pamlandu wogonana ndi...
Sukulu yaukachenjede ya Mzuzu University idasankha chiphadzuwa chonenepa Loweruka sabata yatha pomwe adali ndi chisangalalo chawo cha Social Weekend. Mtolankani...
Pamene nkhani yakupsa kwa misika yayala nthenje m’dziko muno, amalonda ena achita jenkha, kusowa mtengo wogwira katundu wawo atasakazidwa...
Nthawi ino alimi ambiri a fodya ali kalikiriki kufunafuna mbewu, kukonza malo omwe adzalimepo komanso kukonza ndi kufesa nazale....
Dora Nyirenda was born healthy, but everything changed when her father died in 2009. “She stopped talking and just...
Pamene alimi a fodya ali yakaliyakali kukonzekera ulimi wa 2015/16, mlangizi wa zaulimi wa fodya m’boma la Rumphi, Charles Jere,...
Livingstonia Synod of the Church of Central Africa Presbytery(CCAP) through its Deaf Awareness Community Training Project (Deaf ACT) is promoting...
Police in Nkhata Bay have arrested a man for allegedly obtaining money under false pretence. The suspect claimed to work...
The Livingstonia Synod of the CCAP has launched its new and revised hymns in Tumbuka, Kyangonde and Tonga languages. The...
Ngakhale malamulo a dziko lino amakana kumutchula munthu kuti ndi mfiti, Amalawi ambiri amakhulupirira kuti ufitu uliko. Anthu a m’mudzi...
Pamene ena amati chikondi sichiona chikhalidwe kapena mtundu wa khungu la munthu, banja la Manaseh Chisiza, mkulu wa bungwe...
Bambo wina wagundidwa ndi galimoto ku Mzuzu pomwe amathawitsa mapaketi awiri a khofi omwe amamuganizira kuti adaba pa Mzuzu...
Police in Mzimba have engaged the clergy in the fight against crime in the district. The development is in...
Pali mwambi woti ndigwire uku ndi uku pusi anagwa chagada. Penanso amati mapanga awiri avumbwitsa, kutanthauza kuti ndibwino kuchita chinthu...
Mulungu wamva pemphero ndi pembedzero la Paul Kamanga, yemwe ndi mtolankhani, komanso wowerenga nyuzi pa MBCTv—mnyamatayu wadalitsika ndi kachiphadzuwa...
Pamene nkhanza zambiri zomwe zimachita zimakhakla zochokera kwa abambo kupita kwa amayi, Loveness Nakayuni wa m’mudzi mwa Chapyoka, T/A Mwaulambia...