Mfutso mpatali
Chilimwe chikuyandikira ndipo chakudya cha ziweto chili paliponse. Mkulu wa zaulimi wa ziweto m’boma la Kasungu akuti apa ndi pamene...
Chilimwe chikuyandikira ndipo chakudya cha ziweto chili paliponse. Mkulu wa zaulimi wa ziweto m’boma la Kasungu akuti apa ndi pamene...
Minister of Lands Kezzie Msukwa says government is carrying out a customary land registration exercise to ensure that people under...
Akatswiri a zakafukufuku wa mbewu m’dziko muno adafufuza njira ya makono yobzalira mtedza imene ili ndi kuthekera kochulukitsa zokolola za...
Kuonjezera pa kuthawa ng’amba, woona za mbewu za mtundu wa nyemba ku nthambi ya kafukufuku wa zaulimi ya Bvumbwe m’boma...
A study by International Institute of Tropical Agriculture (Iita), which focuses on youth participation in agriculture, has indicated that the...
Padamu limodzi lokha la mamita 20 mulitali ndi 18 mulifupi wakololapo nsomba zolemera makilogalamu 300 atazidyetsera kwa miyezi 5 chakudya...
Minister of Agriculture Lobin Lowe has promised that his ministry will put new regulations in agribusiness that will favour Malawian...
Pamene m’nyengoyi tomato amatsika mtengo chifukwa cha kuchuluka pamsika, katswiri pa luso lopanga zakudya zosiyanasiyana kuchokera ku mbewu za zipatso...
Tomato waufa amasungika kwa zaka ziwiri, mtengo wake ndi golide kale komanso ndiwo zake zimakhala za maonekedwe a pamwamba ....
Atangomva kuti ulimi wa nkhumba ndi waphindu Leckner Kanyama wa m’boma la Lilongwe adayamba ulimiwu mwansangala poganiza kuti atola chikwama....
Chimodzimodzi ulimi wina ulionse, ulimi wa nkhumba uli ndi ndondomeko yake yoyenera kutsatira poweta kuti mlimi apindule. Mphunzitsi wa zaulimi...
Katswiri wa zaulimi wa mbewu za m’gulu la masamba ndi zipatso ku Lilongwe University of Agriculture and Natural Resources (Luanar)...
Pamene alimi ambiri akugulitsa chimanga chouma pa mtengo wotsika, mlimi wa chimanga chachiwisi ku Area 25 m’boma la Lilongwe Kandida...
Agro-industry will play a key role in the creation of one million jobs, which the new government promised Malawians ahead...
Kaitane Shuga wa m’mudzi mwa a Gavi ku Chileka m’boma la Blantyre ndi mmodzi mwa alimi amene amachita ulimi wothirira...
Malingana ndi kuchuluka kwa anthu achikulire amene amabwera pachipatala cha anthu okalamba cha Kalibu Elderly Clinic ku Lirangwe m’boma la...
Chukwu kapena aflatoxin m’Chingerezi ndi liwu lomwe silichoka pakamwa ku ulimi wa mtedza m’dziko muno chifukwa ndi chipsinjo chachikulu ku...
Minister of Gender, Children, Disability and Social Welfare Mary Navicha has warned that her ministry will punish contractors that construct...
Minister of Agriculture, Irrigation and Water Development Kondwani Nankhumwa has asked farmers in the country to diversify their farming to...
Chimodzimodzi akulu, ana nawo amakhala pachiopsezo cha matenda othamanga magazi choncho makolo akuyenera kuwateteza, watero mkulu wa pa chipatala cha...