Minister vows to punish errant contractors
Minister of Gender, Children, Disability and Social Welfare Mary Navicha has warned that her ministry will punish contractors that construct...
Minister of Gender, Children, Disability and Social Welfare Mary Navicha has warned that her ministry will punish contractors that construct...
Minister of Agriculture, Irrigation and Water Development Kondwani Nankhumwa has asked farmers in the country to diversify their farming to...
Chimodzimodzi akulu, ana nawo amakhala pachiopsezo cha matenda othamanga magazi choncho makolo akuyenera kuwateteza, watero mkulu wa pa chipatala cha...
Kuchokera ku phindu la ulimi wothirira, Catherine Bamusi wa m’boma la Blantyre adaganiza zogulako nkhuku zachikuda kuti zizimupatsa manyowa, ndiwo...
Pamene alimi ena akugulitsa ziweto zawo kwa mavenda motsika mtengo, Chawezi Nyirenda yemwe ndi mlimi wa nkhumba ku Lilongwe akupha...
Bungwe la Water for People Malawi (WPM) lomwe cholinga chake n’kuonetsetsa kuti anthu m’dziko muno azimwa madzi aukhondo, komanso kukhala...
M’mwezi wa February chaka chino mlimi wina wa nkhumba m’boma la Lilongwe, Jeofrey Kaiyatsa, adaona ngati malodza nkhumba zake zonse...
Kodi ulimi wa njuchi mudayamba liti? Ulimiwu ndidayamba mu 2017. Nanga chidakukopani n’chiyani? Nditalingalira mozama ndidaona kuti ulimi wa njuchi...
Alfred Mumba wa m’boma la Dowa amalima mbatata pa malo okwana maekala 5. Iye amapeza matumba osachepera 250 a mbatata...
Water for People Malawi (WPM) and Chirazulu District Council have signed a three-year memorandum of understanding (MoU) that will see...
Pamene mbewu ya mtedza yacha, katswiri wa mbewu za mtunduwu kwa Bvumbwe Richard Andasiki akuti alimi ateteze mbewuyi ku chuku...
Woona za mafizo pa chipatala cha anthu achikulire cha Kalibu ku Lilangwe m’boma la Blantyre Veronica Mughogho akuti mafizo ndiothandza...
Katswiri wa ulimi wa ziweto wa ku Lilongwe University of Agriculture and Natural Resources (Luanar) Timothy Gondwe wati kukhala ndi...
Mkulu woona za mbewu za m’gulu la zipatso ku dipatimenti ya za kafukufukuku mu unduna wa zamalimidwe Felix Chipojola akuti...
Mlimi wochenjera monga NELLIE NYONI wa m’boma la Balaka amayambiratu ulimi wa m’chilimwe mvula ikamapita kumapeto kuti asavutike kwambiri ndikuthirira....
Potsatira mvula yochuluka yomwe yagwa m’chakachi, akatswiri a za kafukufuku wa ulimi wa mthirira akuti alimi a m’zigwa za dziko...
Alimi m’madera a dziko lino amakolola chimanga mosiyanasiyana malingana ndi kuzolowera kwawo koma mphunzitsi wa kunthambi ya za maphunziro a...
Mbewu ya chimanga nayo imafuna kuyichengetera nthawi yokolola kuti zokolola zikhale zochuluka ndi zopatsa kaso. Wachiwiri kwa mkulu woona za...
United Nations (UN) Women has moved to lobby for rural women farmers’ access to loans from financial institutions. Speaking yesterday...
Dotolo wa pa chipatala cha Gulupu m’boma la Blantyre, Lerato Mambulu, wati kufa kwa ziwalo nthawi zambiri kumachitika mwadzidzidzi. Pachifukwa...