-
Tikuchita bwanji ndi matewera?
Thewera loti lagwiritsidwa ntchito limaipa mmaso komanso kudetsa kukhosi. Mwina likakhala la mwana wako, komabe ambiri limativuta kuyang’ana, kuligwira…
Read More » -
Chonona chifumira kudzira
Tikamakamba za kufunika kuti pasamakhale kusiyana pa mwayi womwe amayi ndi abambo akupatsidwa, titamakumbuka za mwambi uwu wakuti chonona…
Read More » -
Kuvulaza namfedwa
Ndinali pa maliro ena masiku apitawa komwe amfumu adaganiza zokhutula nkhawa zawo za anamfedwa tili kumanda. Amfumuwo adati sadakondwe…
Read More » -
Kuikira kumbuyo khalidwe loipa
Zimanenedwanenedwa zinthu ngati izi kwa amayi okwatiwa: “Osamasiyira Anaphiri kuti azingophikira abambo, kenaka akulandani banja…” “Osaleka kudzisamalira chifukwa bamboyo…
Read More » -
Kumaona pomvetsera mahedifoni
Malinga ndi kusintha kwa zipangizo zogwiritsa ntchito, moyo ndi makhalidwe a anthu zikunka zisintha tsiku ndi tsiku. Pafupifupi aliyense ali…
Read More » -
‘Boma lisavomereze kuchotsa pathupi’
Potsatira zomwe ndinalemba sabata yatha, mmodzi wa awerengi watumiza maganizo ake motere: Rabecca, Ndine mmodzi mwa amene ndimatsatira…
Read More »