‘Osakondera odya nawo K6.2 biliyoni’
Bota layamba kuwira mumphika wa K6.2 biliyoni yothandiza polimbana ndi matenda a Covid 19 yomwe ikumveka kuti idatafunidwa ndipo akuluakulu...
Bota layamba kuwira mumphika wa K6.2 biliyoni yothandiza polimbana ndi matenda a Covid 19 yomwe ikumveka kuti idatafunidwa ndipo akuluakulu...
Mkokemkoke umene udalipo pakati pa aphunzitsi ndi boma watha tsopano ndipo ophunzira amayenera kubwerera kusukulu dzulo Lachisanu. Izi zadza kutsatira...
Komiti yotsogolera kulimbana ndi matenda a Covid yalengeza kuti sukulu zonse zitsegulidwe Lolemba likudzali pa 22 February. Nduna ya zaumoyo...
Aphungu a Nyumba ya Malamulo ayamba kuunika momwe bajeti ya 2020 mpaka chaka chino yayendera m'miyezi 6 yoyamba Lolemba likudzali...
Pulani ya boma yoti sukulu zikuyenera kutsegulidwanso Lolemba likudzali yasinthidwanso ndipo tsopano Unduna wa zamaphunziro ukufuna kuti uwunikenso m’mene mliri...
Magulu omenyera ufulu wa anthu komanso bungwe la anthu achialubino la Association for People with Albinism in Malawi (Apam) ati...
Churches in the country have asked government to rescue them from financial problems they are experiencing due to restrictions on...
Anthu ambiri akhala akudabwa kuti gulu lomwe lakhala likutsogolera Amalawi pa ziwonetsero zokhudza kusagwirizana ndi momwe boma likuyendera la Human...
Chaka cha 2020 chidali chaka cha pelete chomwe podzuka m’mawa wa tsiku la pa June 27 2020, Amalawi adadzidzimuka kuona...
The first major peaceful demonstration against the Tonse Alliance government took place in Lilongwe yesterday, with hundreds of protestors giving...
Vice-President Saulos Chilima says the country needs quality roads like the Ntcheu – Tsangano Road which is being constructed by...
Yafika nyengo ya zisangalalo za Khrisimasi ndi Nyuwere ndipo ena ayamba kale mapwando pomwe ena akukonzekera masangalalidwe osiyanasiyana monga kupita...
Gulu lomwe lakhala likudzudzula boma la Tonse Alliance chilowereni m’bomamo la Centre for Democracy and Economic Development Initiative (Cdedi) mogwirizana...
The European Union (EU) delegation to Malawi has called on the Malawi Government to join over 142 countries globally that...
Malawi has said the Republic of Korea’s donation of Covid-19 test kits will boost the fight against the pandemic. Minister...
Minister of Agriculture Lobin Lowe has urged chiefs from Lilongwe District to take a lead in the fight against gender-based...
Boma lalamula apolisi m’dziko muno kuti athothe akabaza onse a njinga zamoto zopanda mapepala oziyenereza kuyenda pamsewu ndi kumanyamula anthu....
Pregnancy-related deaths in Malawi remain rampant. According to the Ministry of Health, the country has one of the highest maternal...
Mkati mwa sabatayi mwachitika nkhani zikuluzikulu koma imodzi yomwe yamanga nthenje ndiyo ya banja la mneneri Shepherd ndi Mary Bushiri,...
Alimi omwe chipulumutso chawo cha chaka chino chili pa zipangizo zotsika mtengo m’pulogalamu ya Affordable Inputs Programme (AIP) alila mokweza...