-
National News
Dzaleka refugees get farm inputs boost
Refugees at Dzaleka Camp in Dowa are eyeing bumper yields this season following a boost in farm inputs which…
Read More » -
Chichewa
2017 yatilandira ndi zigumula
Pangotha sabata chilowereni chaka cha 2017, koma malipoti a ngozi zakudza ndi mvula m’maboma osiyanasiyana atopetsa kale. Nyumba, sukulu,…
Read More » -
Chichewa
Aliza abale pa Khrisimasi chifukwa cha mowa
Chaka chilichonse, 25 December ndi tsiku lachisangalalo koma chaka changopitachi lidali lachisoni m’banja la a Moses a kwa Chinthambwe…
Read More » -
Chichewa
Mzungu wolemba dikishonale ya Chichewa
Dikishonale kapena kuti buku lotanthauzira mawu ndi imathandiza anthu kupeza matanthauzo a mawu omwe akuwavuta kuti amvetsetse zomwe nkhani…
Read More » -
Chichewa
Tsala bwino 2016
Pamene tikutsendera chaka cha 2016, akadaulo ena pandale ati zochitika m’chakachi zikutsimikiza kuti Amalawi akuchenjera ndiye andale asamale mu…
Read More » -
Chichewa
‘Tidasala masiku 52 kuti Mulungu atiunikire’
Nthawi zambiri, anthu timatenga banja ngati sitepe pamoyo wathu basi koma tikalingalira momwe banja la m’busa komanso mlembi wa mkulu…
Read More » -
Chichewa
Atenge basi ndani?
Matimu a Nyasa Big Bullets ndi Mighty Be Forward Wanderers Lolemba akhala akukumana pampikisano wa Basi Ipite Soccer Fiesta wolimbirana…
Read More » -
Chichewa
‘Chisangalalo chafika, Samalani kuli mavuto’
Mawa laliwisiri ndi tsiku la Khirisimasi ndipo Lamulungu sabata ya mawa ndi tsiku lokumbukira kulowa chaka cha 2017. Iyi ndi…
Read More » -
Chichewa
‘Pewani ngozi, kuberedwa’
Nyengo ya Khirisimasi ndi Nyuwere kumachuluka ngozi za pamsewu, mchitidwe wa umbava ndi umbanda komanso ngozi zina monga kumira m’madzi…
Read More » -
National News
UN awaits more action on cases against persons with albinism
The United Nations (UN) has said it expects more action from Malawi on cases related to attacks on persons…
Read More » -
Chichewa
Agumula nyumba pokaikira masalamusi
Mbuto ya kalulu idakula ntadzaonani. Mwambiwu udapherezera Lachiwiri ku Lilongwe pomwe anthu okwiya ku Mtsiriza adagumula nyumba ya banja lina…
Read More » -
Chichewa
Gondwe azaza pamsonkhano
Nduna ya za chuma Goodal Gondwe Lolemba idazaza pamwambo wosayinirana pangano la ngongole ndi banki ya zachitukuko mu Africa…
Read More » -
Business News
Young entrepreneurs eye fish market opportunities
Seven Malawian youth groups have secured financial support from the African Entrepreneurship Hub (AEH) to invest in technologies in…
Read More » -
Nkhani
Akwenya woganiziridwa kusowetsa anthu pa KCH
Tsoka sasimba. Mayi wina wa ku Area 25 mumzinda wa Lilongwe adaona zakuda Lolemba lapitali atapita kuchipatala chachikulu cha Kamuzu…
Read More » -
Nkhani
Mafumu asalidwa pogawa chimanga
Ntchito yogawa chakudya kwa anthu osoweratu pogwira ili mkati koma kafukufuku wathu wasonyeza kuti mafumu sakukhutira ndi momwe ntchitoyi ikuyendera…
Read More » -
Nkhani
Tionana 2019— Mafumu
Mafumu achenjeza kuti aphungu omwe sakufuna kumva madandaulo awo pankhani ya lamulo lokhudza malo a makolo adzakumana ndi chipande pachisankho…
Read More » -
National News
School feeding programme increases enrolment in Salima
Enrolment in 10 primary schools of Traditional Authority (T/A) Khombedza in Salima has increased from an average of 700…
Read More » -
Nkhani
Aphungu aunguza njira zokhaulitsira auve
Uve wanyanya m’dziko muno koma pano zafika poti wina akalowa nazo kundende! Nyumba ya Malamulo yati nyansi zamgonagona zomwe zili…
Read More » -
Editors Pick
Malonda a fodya aliritsa alimi ena
Chikadakhala chimanga bwenzi akusimba lokoma, koma poti ndi fodya oyimba adalasa ponena kuti ikulirenji ntchito, chaka ndi chaka alimi…
Read More » -
National News
Islamic body boosts agriculture at Maula Prison
Association of Sunni Madrasah (Asum) has handed over K1.5 million agriculture equipment to Maula prison in Lilongwe to help…
Read More »