-
Pa Wenela pasintha zedi
Tsikulo pa Wenela padali fumbi. Lazalo Watsika wabwera ndi moto ndithu. “Abale inu, dzikotu ili limatembenuka zedi. Ndani ankadziwa kuti…
Read More » -
Chichewa
Ndithu chili ndi mwini
Kusankha Balaba Kumukana Yesu Usapange mistake, chonde chonde Nyimbo ya Evans Meleka idali kuphulika pa Wenela tsiku limenelo. Ya Ndirande…
Read More » -
Chichewa
Sitalaka pa Wenela
Lidali Lachinayi usiku ndipo tidali malo aja timakonda pa Wenela kukambirana izi ndi izo. Adachuluka adali madilaivala ndi makondakitala a…
Read More » -
Koma pa Wenela zidzatheka?
Tsikulo tidakhala pa Wenela. Tidali kusowa cholankhula. Kodi ndi January ameneyu? Ayi ndithu. Kukazinga chimanga chisanachoke m’munda. Nyimbo zomwe ankaika…
Read More » -
Chichewa
Kulingalira malumbiro
Abale anzanga, tidakhala pa Wenela kuonera kulumbiritsa kwa atsogoleri. Woyamba kulumbiritsidwa adali Adama Barrow wa ku Gambia. Musandifunse kuti ameneyu…
Read More » -
Basi ayisempha
Tsiku limenelo sitidakhale pa Wenela. Palibe ojiya, osolola, osenza ndi oitanira amene adatsala pa Wenela. Tidakwera galimoto la mkulu wina…
Read More » -
Basi ayisempha
Tsiku limenelo sitidakhale pa Wenela. Palibe ojiya, osolola, osenza ndi oitanira amene adatsala pa Wenela. Tidakwera galimoto la mkulu wina…
Read More » -
Khirisimasi ya Niko
Nthawi ija yafikanso. Niko adali pa Wenela tsiku limenelo Abale anzanga, ndikuthokoza Mulungu amene wandilola kuti ndifike tsiku la…
Read More » -
Malingaliro a Khirisimasi
Khirisimasi ndi Januwale Zalowa m’manyumba (adalakwitsa ndi oimbayo osati in Tadeyo) Zaseseratu! Kwa amene adaliko nthawi imene Kennedy Ndoya, ankatchuka…
Read More » -
Chichewa
Akhalenso ndi moyo wautali
Tsiku limenelo ndidakwiya zedi pa Wenela. Mkwiyo wanga udali waukulu zedi moti ndidafuna kuphulika. Inde, udali mkwiyo waukulu zedi…
Read More » -
Chichewa
Msika wa ziwala, mbewa
Tidali pamalo aja timakonda pa Wenela, mnyamata uja Bonny Wasawaliya Kanindo atafika ku nyumba ya ulemu ku Nyumba ya…
Read More » -
Chichewa
Zovula pa Wenela ayi, tamva!
Tsikulo pa Wenela padali ziii! Moti ojiya, osolola ndi osenza onse adali khumakhuma. Ndalamatu ndalama zalowa ku silent ndiye…
Read More » -
Chichewa
Aphungu avuta
Tsikulo pa Wenela padali ziii! Moti ojiya, osolola ndi osenza onse adali khumakhuma. Ndalamatu, ndalama zalowa ku silent ndiye…
Read More » -
Chichewa
One-man demo pa Wenela
tsikulo pa wenela padaterera. zidaliko. nkhani idavuta ndi ija tidaiyamba sabata yatha. Inde, iyi nkhani yophana chisawawa, makamaka kwa…
Read More » -
Chichewa
Kulakwa, kulakwatu pa Wenela!
Tsikulo lidali lokumbukira asungwana ndi amayi oyendayenda ndipo tidazunguliradi mumzinda wa Lilongwe. Tidali ndi Abiti Patuma kuti ationetse monse.…
Read More » -
Chichewa
Ntchentchefly zivuta ku Lilongwe
Tsiku limenelo tidakhala pa Wenela ndipo Abiti Patuma adati tipite ku Lilongwe kumenetu ndalama zabooka malinga ndi ungano wa aphungu…
Read More » -
Malamulo Khumi pa Wenela
Tsikulo Moya Pete adadabwitsa tonse. Adafika kumalo otsegulira msonkhano wa ana aja amalimbana za ziii! chaka ndi chaka ati…
Read More » -
Chichewa
Mpando Wamkulu afika pa Wenela
Abale anzanga, tsikulo kudali nyimbo zija zogawa tonse pa Wenela. Adayamba ndi Patience Namadingo, yemwe waimba Nyimbo yotamanda uja mneneri…
Read More » -
Chichewa
Za kulephereka kwa zisankho
Muzina Edi mwana Edi sebe santu Muzina zizata mfana Ya muzina Sindikudziwa ngati Papa Wemba nyimboyo adaimverapo koma ndimo ndinkayimvera…
Read More » -
Chichewa
Awiri afa ndi bibida ku KK
Abambo awiri amwalira ndi mowa wa kachaso m’njira zofanana koma malo osiyana m’boma la Nkhotakota. Mneneri wa polisi m’bomali, Williams…
Read More »