Religion News

Hosanna! Hosanna! Mwana wa Davide

Listen to this article

Jerusalem_closeupSabata yapitayi idali yoyera kwa Akhristu, pamene amakumbukira masautso ndi mazunzo amene Yesu Khristu adakumana nawo. Yesu adapachikidwa pamtanda m’manja mwa Pilato ndipo Akhristuwo amakumbukira za imfa yake pamtanda Lachianu Loyera, limene chaka chino lidali Lachisanu langodutsali. Kukumbukirako kudayambika Lamulungu lapitalo pomwe Akhristu amakumbukira za kulowa kwa Yesu mu Yerusalemu pabulu. Apa tikuona Akhristu a ku Kanjedza kuyerekeza momwe zidalili panthawiyo.

Related Articles

Back to top button
Translate »