Nkhani

Madzi siosewera nawo, maka nthawi yamvula

Listen to this article

Madzi ndi moyo, chifukwa amatithandiza m’zambiri. Koma kupanda kusamala, madzi omwewo amadzetsa imfa.

Imfa zina za ngozi zamadzi zikhoza kupewedwa. Mayi ali apayu adayenera kusamala chifukwa malo akuchapawo ndiwoopsa.

Uwutu ndi mtsinje wa Maperera ku Chikhwawa ndipo kuopsa kwake sikuti kungadze pamene mvula yayamba kugwa pafupi ndi mayiyo.

Mvulatu ikhoza kugwa yambiri kumtunda kwa mtsinjewu, mayiyo osadziwa, kenako kumukokolola limodzi ndi mwanayo.

Kusamala n’kofunika.

Related Articles

Back to top button
Translate »