Nkhani
-
Apulumuka lokumbakumba atadya chiphe kuyesa mpama
Anthu 15 a m’mudzi wa Kalonga mfumu yaikulu Mlolo koma anasamukira kwa Milton TA Mbenje m’boma la Nsanje Lamulungu abwerera…
Read More » -
Khonsolo idandaula za mowa wa ‘Ambuye n’tengeni’
Imodzi mwa nkhani zimene zidayala nthenje sabata yatha ndi ya anthu 8 omwe adamwalira kwa Manase mu mzinda wa Blantyre…
Read More » -
‘Osasekerera aphunzitsi ofuna za dama ndi atsikana’
Bungwe loona za maphunziro la Civil Society Education Coalition (Csec) lapempha boma kuti lisalekere panjira kufufuza nkhani yokhudza aphunzitsi ena…
Read More » -
Chepetsani madyo ku maliro
Zimaoneka ngati nkhambakamwa. Umva adzukulu akana kukumba kumanda chifukwa ndiwo sizinali za nyama. Mbali inayi mafumu kukana kuyendetsa mwambo chifukwa…
Read More » -
Amayi ena agundika nkhanza
Tikamakamba nkhani za nkhanza, nthawi zambiri chala chimaloza abambo. Akati nkhani yogwiririra ndi abambo, kaya ndi yomenya, amene amachita izi…
Read More » -
8 akulimbirana wachiwiri kwa mtsogoleri wa MCP
Ulendo wa ku kovenshoni ya chipani cha Malawi Congress Party (MCP) watentha pomwe mamembala ochuluka asonyeza khumbo lodzapikisana nawo m’mipando…
Read More » -
Aphungu akwangula
Aphungu a Nyumba ya Malamulo adakwangula zokambirana zawo dzulo Lachisanu atadutsitsa bajeti yokwana K5.98 triliyoni yomwe akadaulo adati ithandiza kusoka…
Read More » -
Akuti bizinesi yogulitsa mabomba ndiyotentha
Kunjakutu kukuchitika malonda osiyanasiyana. Ena akugulitsa mtedza, mbatatesi kapena nthochi bola apezepo phindu ngakhale lichepe. Komatu pali anthu ena omwe…
Read More » -
Mankhwala akumabedwa bwanji m’zipatala?
Zikuoneka kuti dziko lino latha nzeru pa nkhani zobedwa mankhwala m’zipatala. Ngati njira yothandiza kuthetsa mchitidwewu, panakhazikitsidwa makomiti m’zipatala zonse…
Read More » -
Galu wakuda wadutsa
Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ati maboma 23 a m’dziko muno alibiletu chakudya kotero apempha akufuna kwabwino kuti…
Read More » -
Bajeti ya chaka chino yavomerezedwa
Nyumba ya Malamulo yavomereza bajeti ya ndalama zokwana K5.998 thililiyoni yoti boma ligwiritse ntchito kuyambira pa 1 April 2024 mpaka…
Read More » -
Dikirani kauniuni wachiwiri wa mbewu
Unduna wa za malimidwe wati anthu asathyolere khosi zotsatira za kauniuni woyamba wa mbewu chifukwa kauniyo sadalingalire za ng’amba yomwe…
Read More » -
Sakufuna awakanize kuima
Mamembala ena a chipani cha Malawi Congress (MCP) akutsutsana ndi maganizo amene komiti yaikulu ya chipanicho (NEC) idamanga kumsonkhano wake.…
Read More » -
Anjata wofuna kugulitsa mwana wake
A Chimwemwe Zololo atha masiku 6 m’chitokosi cha apolisi ku Zomba powaganizira kuti amafuna kugulitsa mwana wompeza. A Zololo akuyembekezereka…
Read More » -
Wa zaka 15 amuganizira kupha mchemwali wa 26
Mwana wa zaka 15 ali m’manja mwa apolisi ku Mangochi pomuganizira kuti adazimitsa mchemwali wake wa zaka 26 pa mkangano…
Read More » -
Ululu podula cha unzika
Walira mvula waliranso matope. Anthu amene amalakalaka atapeza chiphaso cha unzika mwayi wawagwera koma ayenera akhetse thukuta kuti izi zitheke.…
Read More » -
A Chakwera alephera kukwaniritsa lamulo lawo lomwe
Akatswiri pa nkhani za chuma ndi ufulu wa anthu adzudzula mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera kaamba kolephera kukwaniritsa…
Read More » -
Aonjezera aphungu
Bungwe loyendetsa zisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) latsutsa mphekesera yoti layamba laimika kaye chilinganizo choonjezera madera a aphungu pa…
Read More » -
Msungwana adakokera boma kukhoti
Chaka cha 2023 chikupita ndi nkhani zake, imodzi mwa nkhani zimene zidayala nthenje ndi ya msungwana wa zaka 14 yemwe…
Read More » -
Mfumukazi ichereza mayi wobereka ana 5 pa kamodzi
Mkazi wa Inkosi ya Makhosi Gomani V, Inkosikati Rishaladza Khanyisa Gomani wati kuchuluka kwa mimba za ana achichepere kukukolezera kusachita…
Read More »