Nkhani
-
Kutentha kwa mnanu kunkira
Nthambi ya za nyengo ya Department of Climate Change and Meteorological Services (DCCMS) yati kutentha kwa mnanu komwe kwakhala kuoneka…
Read More » -
Unicef ilipilira asungwana 5 600 fizi
Asungwana 5 600 omwe akadalephera sukulu kaamba ka vuto la fizi achita mwayi ndi lonjezo la bungwe la United Nations…
Read More » -
Mkonono wanyanya kotsutsa
Akadaulo pa nkhani zosiyanasiyana m’dziko muno ati mbali yotsutsa boma ili ndi benthu lake pa mavuto omwe Amalawi akudutsamo chifukwa…
Read More » -
Amanga mbusa wofuna kupumira pa mwana
Khoti la majisitileti m’boma la Dowa lamanga mbusa wina Bonwell Sinoya wa zaka 36 kukagwira ntchito yakalavula gaga kwa zaka…
Read More » -
Malawi wauma
Vuto la mafuta a galimoto lomwe lanyanya tsopano lakweza mkwiyo mwa Amalawi kaamba kakukwera kwa mtengo wa galimoto zonyamula anthu…
Read More » -
Ulendo wotsiriza wa a John Tembo
Thupi la mphangala pa ndale a John Tembo lidalowa m’manda Lachitatu ku mudzi kwawo kwa Kaphala kwa T/A Kachere ku…
Read More » -
Ma rodibuloku abwerere
Kadaulo pa za chitetezo a Loti Dzonzi omwe adakhalako mkulu wa apolisi ( I G ) m’dziko muno waunikira kuti…
Read More » -
A Tembo asiya Amalawi m’misozi
Imfa ya mphangala ya ndale a John Zenus Ungapake Tembo yaonetsa kuti Amalawi ndi amodzi ngakhale kusiyana kwa zipani za…
Read More » -
Liwu la mafumu pa zochotsa anthu 1 miliyoni mu AIP
Mafumu apereka maganizo osiyanasiyana pa ganizo la boma lochotsa maina 1 miliyoni mu pulogalamu ya zipangizo za ulimi zotsika mtengo…
Read More » -
Boma likugwiritsa K3 biliyoni pothandiza ochotsa mimba
Dziko la Malawi likugwiritsa ntchito pafupifupi K3 biliyoni pa chaka popereka thandizo kwa amayi amene anachotsa mimba pogwiritsa ntchito njira…
Read More » -
Gogo athawa m’mudzi mwake
Abale a gogo Binwell Chabwera amene adathawitsidwa pomuganizira kuti adapha mdzukulu wake m’matsenga anenetsa kuti iwo sakufunanso kuona gogoyo. Gogo…
Read More » -
Zaka ziwiri kwa akuba pa foni
Bwalo la Nsanje Third Grade Magistrate lalamula amuna awiri kukagwira ukaidi kwa miyezi 24 atawapeza wolakwa pa mlandu woba mafoni.…
Read More » -
Alimi akhutira ndi chionetsero
Alimi ena amene afika ku chionetsero cha ulimi chimene nduna ya za malimidwe a Sam Kawale adatsegulira dzulo mu mzinda…
Read More » -
Aphungu akwangula zokambirana
Pamene aphungu a Nyumba ya Malamulo amayembekezeka kukwangula zokambirana zawo dzulo, mkulu wa bungwe loona za ufulu wa anthu la…
Read More » -
Ng’anga zaithina itakanika kudzutsa munthu wakufa
Ng’anga ina ku Balaka yapereka chindapusa cha K90 000 kupewa kukaseweza miyezi 15 imene adamugamula atapezeka wolakwa pa mlandu woti…
Read More » -
Misika ya Admarc siyitsegulidwa msanga
Nduna ya za malimidwe a Sam Kawale ati kampani yogula mbewu ya Admarc siyitsegulidwa kuti iyambe kugula mbewu pokhapokha anthu…
Read More » -
Zaka 59 pa ufulu tapindulanji
Kadaulo pa ndale a George Phiri ati palibe chifukwa chomveka choti dziko la Malawi lizikondwerera ufulu wodziimirira palokha chifukwa m’zambiri…
Read More » -
Aphana pachibale kaamba ka malo
Apolisi m’boma la Lilongwe amanga abambo atatu a banja limodzi powaganizira kuti adapha mbale wawo polimbirana malo m’mudzi mwa Maliseni…
Read More » -
Loans board struggles to recover K16bn
The Higher Education Student’s Loans and Grants Board (HESLGB) says it is struggling to recover K16 billion from its beneficiaries.…
Read More » -
Mlandu wa a Bushiri ukhalako pa Julayi 10
Mlandu wa a Pulofeti Shepherd Bushiri ndi akazi awo a Mary unalephereka kuyamba Lachiwiri kaamba ka kusagwirizana kumene kunalipo pakati…
Read More »