Nkhani
-
Zipani zigonjera chiletso cha Escom
Zipani za ndale m’dziko muno zagwirizana ndi chiletso cha bungwe loyendetsa ntchito za magetsi m’dziko muno la Escom choti zipani…
Read More » -
Kukokana pa za amayi ovina
Zusamvana komwe kudabuka pa zakayendetsedwe ka bungwe la Asilamu la Muslim Association of Malawi (MAM) kwayamba kufalikira m’maboma ambiri tsopano.…
Read More » -
Zimbalangondo zikhapa achitetezo
Anthu akugona khutu lili kunja, tulo tayamba kusowa, chitetezo chatekeseka ku Soche mumzinda wa Blantyre komwe zimbalangondo zatikita achitetezo a…
Read More » -
Mafumu atekeseka ndi bilu ya malo
Mafumu ena m’dziko muno aopseza kuti achita zionetsero ngati lamulo lokhudza malo lingasinthe kuti iwo asakhalenso ndi mphamvu pogawa malo.…
Read More » -
Zipani zilonjeza kampeni yotentha
Pomwe bungwe la chisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) latsala pang’ono kulengeza tsiku loti kampeni pokonzekera chisankho cha pulezidenti wa…
Read More » -
Kuphunzira chingerezi tsono chiziyambira m’Sitandade 1
Angapo mwa makolo m’dziko muno ati ndi okondwa ndi ndondomeko yatsopano yomwe unduna wa maphunziro m’dziko muno wakhazikitsa kuti ana…
Read More » -
K10 000 kwa ophunzitsa kumidzi
Aphunzitsi akumidzi ayembekezere zokoma boma litakwenza ndalama yomwe limawapatsa powalimbikitsa kugwira ntchito kumidzi kuchoka pa K5 000 kufika pa K10…
Read More » -
Kafukufuku wa cashgate sadayankhe
Mabungwe omwe si aboma ati zotsatira za kafukufuku wa kubedwa kwa ndalama za boma (cashgate) kulikulu la dziko lino zomwe…
Read More » -
Mashado a PP ndiwo agawe chimanga cha boma
Anthu amene satsatira chipani cha PP ali pachiopsezo chosumbudzuka ndi njala pamene boma lauza mashado a PP kuti ayambe kugawa…
Read More » -
Kusakaza kudaimitsa zinthu
Bungwe loyang’anira zaufulu wa anthu la Malawi Human Rights Commission (MHRC) lati kusokonekera kwa kayendetsedwe ka chuma cha boma kudapangitsa…
Read More » -
Mvula iwononga katundu ku Phalombe
Inde mvula ndi madalitso, komabe kwa anthu a ku Phalombe ndi Mulanje madalitsowa akuwalandirira kulimba. Ngozi zogwa mwadzidzidzi zafika pena…
Read More » -
‘Cashgate’ isokoneza khisimisi kwa a m’boma
Anthu ambiri ogwira ntchito m’boma ali pachiwopsezo chakuti Khisimisi ya chaka chino saiwona bwino chifukwa chosowa ndalama anthu ena ogwira…
Read More » -
MESN ikufuna kuwerengera kwapadera
Mgwirizano wa mabungwe a zachisankho la Malawi Electoral Support Network (Mesn) lati likumenyerera mabungwe ena kuti lidzakhale ndi malo apadera…
Read More » -
Mandela alowa m’manda mawa
Thupi la mtsogoleri woyamba wachikuda wa dziko la South Africa, Nelson Mandela, likuyembekezeka kulowa m’manda mawa kumudzi kwawo ku Qunu…
Read More » -
Mwaulambia alowa m’manda lero
MtThupi la Senior Chief Mwaulambia ya m’boma la Chitipa imene idatisiya Lachiwiri likuyembekezeka kulowa m’manda lero. Mwana wa mfumuyo Briston…
Read More » -
‘JB asabisalire kwa amphawi za kuyenda’
Mtsogoleri wa dziko lino Joyce Banda wamenyetsa nkhwangwa pamwala ponena kuti, zivute zitani, sangasiye kuyendera anthu m’midzimu ndipo wati zikafika…
Read More » -
Ku Zomba abwekera feteleza wa mbeya
Pa Bungwe la Millennium Villages Projects (MVP) lati nthawi yakwana pamene alimi akuyenera kukolola pogwiritsa ntchito feteleza watsopano wotchedwa Mbeya…
Read More » -
‘Lamulo la chuma cha pulezidenti liunikidwenso’
Mmodzi mwa akatswiri a za malamulo Edge Kanyongolo wati lamulo lomwe likukamba za katundu ndi chuma cha atsogoleri a dziko…
Read More » -
Ntchito yomanga njanji ya ku Nkaya yaima
Ntchito yomanga njanji yochoka ku Kachaso kupita ku Nkaya ayiimitsa mpaka kampani ya Mota-Engel ndi ogwira ntchito kukampaniyo atamvana chimodzi.…
Read More » -
Mgwirizano wabooka?
Amati “apolisi tisamawanyoze ndi abale athu”, koma zayambika m’dziko muno ndi chipolowe pamene anthu akuthotha apolisi ndi kusasula ofesi zawo…
Read More »