Nkhani
-
Womukaikira zopakula ku Kapitolo adzipereka
Wabizinesi Osward Lutepo, amene wakhala akusakidwa ndi apolisi a dziko lino, komanso polisi ya maiko osiyanasiyana ya Interpol, Lachitatu adatera…
Read More » -
Kupha nyani sayang’ana nkhope
Kuyambira pomwe dziko lino lidayamba kukhala ndi ulamuliro wa demokalase (matipate) zinthu pang’onopang’no zidayamba kusokonekera, makamaka pakayendetsedwe ka chuma. Muulamuliro…
Read More » -
Umphawi ulikonso kutauni—mtsutso
Ngati munali ndi malingaliro oti muchoke kumudzi ndi kukatambalala kutauni kuti mwina ndiko kuli msipu wobiriwira, iwalani ndithu chifukwa kumeneko…
Read More » -
Kodi za Gaba zalowa?
M’sabatayi aganyu tidali osangalala kumva kuti chilombo cha ukonde, Gabadihno Mhango, mwana wa Flames, tsopano wayamba kusewerera m’timu yatsopano ya…
Read More » -
Kusolola m’boma kudayamba kale
Zayamba kuululika. Kafukukufuku yemwe adapangidwa pakati pa 2009 ndi 2012 waulula kuti boma lotsogozedwa ndi chipani cha DPP, chomwe mtsogoleri…
Read More » -
Kampani yatsopano ikatamutsa alimi
Kampani yatsopano yogula ndi kugulitsa zakumunda ya Auction Holdings Limited Commodities Exchange (AHCX) yamema alimi kuti akagulitse mbewu zawo kubungweli…
Read More » -
Kugwiririra ana kudzatha?
Pafupufupi tsiku lililonse tikumamva kapena kuwerenga malipoti akuti mwana wagwiririridwa penapake. Omangidwa akumangidwa. Kugwira ndende ndiye kosakamba koma zikuoneka kuti…
Read More » -
Kupakula kukapitolo, JB achotsa nduna
Mtsogoleri wadziko lino Joyce Banda Lachitatu adakana kupumitsa mamulumuzana ena aboma kutsatira kupakula ndalama za boma kumene kwanyanya kulikulu la…
Read More » -
A ku Mozambique akulembetsa mavoti
Nzika zina za m’dziko la Mozambique zikulembetsa nawo m’kaundula wa mavoti ku Dedza popofuna kuti zidzavote nawo pa chisankho cha…
Read More » -
Banda adataya mwayi
Mtsogoleri wa dziko lino Joyce Banda adataya mwayi wosonyeza bwino lomwe kuti akudziwa chimene akuchita polimbana ndi chiwanda chidalowa kulikulu…
Read More » -
Mugwiliranji bere la mwini?
Masiku apitawa mtsikana wina adandifotokozera za momwe mphongo ina idagwirira bere lake pa msewu mumzinda wa Lilongwe. Mtsikanayu adali akungodziyendera …
Read More » -
Nam yapindulanji pa Tigresses?
Bungwe la Malawi National Council of Sports tsopano layeretsa timu ya Tigresses kuti Nam ndiyo yolakwa pankhani yoti timuyi ichotsedwe…
Read More » -
Papsa tonola, kusolola kwaphweka ku Kapitolo
Kwagwa papsa tonola kulikulu la dziko lino (Capital Hill) ku Lilongwe komwe akuluakulu ena ogwira ntchito zowerengera chuma cha boma…
Read More » -
‘Makuponi si yankho, ingosiyani’
Ngakhale boma lili kalikiliki ndi ndondomeko ya zipangizo zotsika mtengo, mphunzitsi wa zandale Joseph Chunga komanso mkulu woona zaufulu wachibadwidwe…
Read More » -
‘Chimanga cha 10kg tidyapo kangati’
Anthu ena akwiya m’dziko muno ndipo apempha boma kuti lisinthe ganizo lake lolamula bungwe la Admarc kuti lizigulitsa chimanga chosapitirira…
Read More » -
Chalaka Kinnah Tom sangatole
Aganyu tidagwiritsidwa utsi titalonjezedwa ndi yemwe anali mphunzitsi wa Flames Tom Santfiet kuti Flames ikavulaza Nigeria. Nigeria idatiumbudza 2-0. Iye…
Read More » -
Phalombe yakonzeka kuthana ndi ngozi
Pafupifupi chaka chilichonse boma la Phalombe limakumana ndi ngozi zachilengedwe, kuthana ndi mavutowa lakhala vuto kwa zaka. Mwachitsanzo, chaka chatha…
Read More » -
Kusamala ndi antchito olera ana
Ana ambiri masiku ano akuleredwa ndi antchito m’makomomu popeza makolo awo amakhala otangwanika kusaka makobidi kuntchito kapena mabizinezi. Ndipo alipo…
Read More » -
Zitukuko zothandiza Amalawi zisamafe
Patha zaka 50 kuchokera pamene dziko lino lidalandira ufulu wodzilamulira. Tikaunikira bwino momwe chuma chikuyendera m’dziko muno poyerekeza ndi momwe…
Read More » -
Ndale zosadula chitukuko zikhumudwitsa aMalawi
Kudula ntchito zimene adayambitsa atsogoleri akale a dziko lino kukuchititsa kuti Amalawi azingosaukirabe chifukwa ndalama zambiri zimangolowa m’madzi ntchitozo osamalizidwa.…
Read More »