Boma, mafumu salabadira mavuto a Amalawi
Kusapezeka kwa boma komanso mafumu ku zokambirana zomwe adaitanitsa a bungwe la amipingo la Public Affairs Committee (PAC) sabata yatha...
Kusapezeka kwa boma komanso mafumu ku zokambirana zomwe adaitanitsa a bungwe la amipingo la Public Affairs Committee (PAC) sabata yatha...
Kubwera kwa ndalama ya K1 000 yogwirana ndi chisonyezo kuti zinthu sizili bwino pa chuma m’dziko muno, atero akadaulo a...
Katswiri pa ndale yemwe ndi mphunzitsi wa phunziro la ndale kusukulu ya ukachenjede ya Chancellor College, Joseph Chunga wati machokedwe...
Anthu m’midzi ingapo m’boma la Mwanza akunyanyala ntchito zachitukuko pokwiya ndi ganizo la mfumu yayikulu T/A Kanduku loti Achewa m’dera...
Mpingo wa katolika wapempha Amalawi kuti apempherere dziko la Malawi ndi utsogoleri wadziko lino panyengo ya Lenti. Muuthenga wake wanyengoyi,...
Kusamvera mabwalo a milandu komwe boma laonetsa kwasonyeza kulephera kwa chipani cha Democratic Progressive (DPP) pa kulemekeza ufulu wachibadwe, zomwe...
Pali chiyembekezo kuti ntchito za mtengatenga za m’dziko muno zingapite patsogolo chifukwa ntchito zikuluzikulu za chitutuko cha misewu zoposa zisanu...
Mgwedegwede womwe wayanga chipani cholamula cha DPP ndi zina zotsutsa boma monga UDF ndi MCP ungabale zisankho zabwino mu 2014,...
Mafumu komanso anthu m’dziko muno ati ndiokhumudwa ndi zomwe oganiziridwa kuti ndi mavenda m’mizinda wa Lilongwe, Blantyre ndi Mzuzu m’sabatayi...
Mavenda 40 omwe adamangidwa mu mzinda wa Lilongwe sabata yathayi ali m’gulu la anthu zikwizikwi za anthu amene akhudzidwa ndi...
Anthu m’madera osiyanasiyana m’sabatayi ati kuchoka kwa phungu wa chipani cholamula cha DPP m’dera la ku m’mawa m’boma la Blantyre,...
Chipasupasu cha m’chipani chakale cholamula cha United Democratic Front (UDF) chingaopseze ulamuliro wa demokalase m’dziko muno womwe umalira kuti pakhale...
Mkulu wa bungwe loona ufulu wa ogula la Consumers Association of Malawi (Cama), John Kapito wati boma likuyenera kutulutsa chimanga...
Pa 25 Disembala chaka chilichonse Akhristu padziko lapansi amakumbukira kubadwa kwa Yesu. Tsikuli ndi mawa laliwisili. M’malo ambiri m’nyengoyi, chisangalalochi...