Thirani feteleza nthawi Yabwino, moyenera
Mlimi akhoza kukonza m’munda moyenera, kubzala mbewu yabwino ndi moyambirira komanso kuthana ndi tchire koma osapeza zokolola zoyenera akaphonya pankhani...
Mlimi akhoza kukonza m’munda moyenera, kubzala mbewu yabwino ndi moyambirira komanso kuthana ndi tchire koma osapeza zokolola zoyenera akaphonya pankhani...
Yafika nyengo ya zisangalalo za Khrisimasi ndi Nyuwere ndipo ena ayamba kale mapwando pomwe ena akukonzekera masangalalidwe osiyanasiyana monga kupita...
Gulu lomwe lakhala likudzudzula boma la Tonse Alliance chilowereni m’bomamo la Centre for Democracy and Economic Development Initiative (Cdedi) mogwirizana...
Kucha kwa Lolemba lapitali Amalawi adadzuka ndi nkhani yododometsa kuona adindo (makhansala) akulalata poyera kudelera alawansi ya K20 000 ndipo...
Boma lalamula apolisi m’dziko muno kuti athothe akabaza onse a njinga zamoto zopanda mapepala oziyenereza kuyenda pamsewu ndi kumanyamula anthu....
Ndili pa moto Gogo, Ndili pa ubwenzi ndi mtsikana wina yemwe amaphunzitsa pa sukulu ina ya pulayimale ya mu mzinda...
Themba William Mwale adamuona koyamba Grace Kadzakumanja kumalo a zochitikachitika a Bingu International Convention Centre (BICC) komwe onse ankakatola nkhani....
Gogo, Ndili pa banja ndipo tili ndi mwana mmodzi. Koma vuto ndi loti anthu anawanamiza amuna anga kuti ndili ndi...
Akatswiri a zakafukufuku wa mbewu m’dziko muno adafufuza njira ya makono yobzalira mtedza imene ili ndi kuthekera kochulukitsa zokolola za...
Kuonjezera pa kuthawa ng’amba, woona za mbewu za mtundu wa nyemba ku nthambi ya kafukufuku wa zaulimi ya Bvumbwe m’boma...
Mkati mwa sabatayi mwachitika nkhani zikuluzikulu koma imodzi yomwe yamanga nthenje ndiyo ya banja la mneneri Shepherd ndi Mary Bushiri,...
Alimi omwe chipulumutso chawo cha chaka chino chili pa zipangizo zotsika mtengo m’pulogalamu ya Affordable Inputs Programme (AIP) alila mokweza...
Akufuna mwana Gogo, Ndakhala m’banja ndi mwamuna wanga zaka zisanu, koma wopanda mwana. Mwamuna wanga amalimbitsa mtima kuti ndisadandaule popeza...
Eric Aniva yemwe adaseweza chifukwa chokhala fisi ku Nsanje wati akulingalira zosumira boma pomugwiritsa jere chonsecho amangotsatira chikhalidwe. Aniva, yemwe...
Padamu limodzi lokha la mamita 20 mulitali ndi 18 mulifupi wakololapo nsomba zolemera makilogalamu 300 atazidyetsera kwa miyezi 5 chakudya...
Sabata ino JAMES CHAVULA akupitiriza kucheza ndi Timothy Mtambo nduna ya zophunzitsa anthu zosiyanasiyana komanso umodzi. Sabata yatha, iye adatambasula...
Pamene mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera Lachitatu adakhazikitsa ntchito yoti Amalawi azichotsa zinyalala m’madera awo, akadaulo a zachilengedwe ati...
Munthu akafika poderera ntchito ndi kusankha ulimi ndiye kuti akupezamo phindu la mnanu. Magdalene Juma Mambiya wapeza chonde mu ulimi...
Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera walamula bungwe loona za mayeso la Malawi National Examinations Board (Maneb) kuti lifufuze chomwe...
Amalawi ena ayamba kugula feteleza ndi mbewu zotsika mtengo koma madera ena ngakhale maina a opindula pa chilinganizochi sanadziwike. Sabata...