Chichewa
-
Aphunzitsi adzawalabadire ndani?
Ambiri timadzudzula kujombajomba komanso kusalimbikira ntchito kwa aphunzitsi m’sukulu za boma. Mchitidwewu ngopititsa pansi maphunziro chifukwa ophunzira amachoka kusukulu asanasulidwe…
Read More » -
Scova adatani?
Nkhani yavuta m’sabatayi ndi ya Nyerere kuti zidagenda pomwe zimasewera ndi Blue Eagles. Aganyu sitivomereza kugenda ndipo tafuna timvetsetse chomwe…
Read More » -
Ntchito yomanga njanji iima
Ntchito yomanga njanji yochoka ku Kachaso kupita ku Nkaya ayiimitsa mpaka kampani ya Mota-Engel ndi ogwira ntchito kukampaniyo atamvana chimodzi.…
Read More » -
Mandela adwala mwa kayakakaya ku South Africa
Mtsogoleri wakale wa dziko la South Africa Nelson Mandela adali kudwalika zedi pachipatala china ku Pretoria m’dzikomo. Pomwe timasindikiza Tamvani…
Read More » -
‘Lamulo la chuma cha pulezidenti liunikidwenso’
Mmodzi mwa akatswiri a za malamulo Edge Kanyongolo wati lamulo lomwe likukamba za katundu ndi chuma cha atsogoleri a dziko…
Read More » -
Mayi athokoza ataomboledwa
Maness Thom wa Zaka 65 wathokoza bungwe losakhulupirira kuti kunjaku kuli Mulungu komanso mphamvu za mizimu ina la Association of…
Read More » -
Wa zaka 70 wofuna kugwiririra amangidwa
Bwalo lamilandu la Dedza Lachiwiri lagamula gogo wa zaka 70 kuti akaseweze kundende zaka zinayi kaamba kofuna kugwiririra mdzukulu wake…
Read More » -
Nanga wapolisi ataphofomoka?
Masiku ano sichikhala chachilendo kuona apolisi atakwera galimoto mosayenera. Ngakhale ntchito yawo n’kuonetsetsa kuti malamulo akutsatidwa, ngakhale pamsewu, apolisiwo ndiwo…
Read More » -
Kudziongola ngati zenizeni, koma ayi
Lachitatu sabata yatha anyamata a Flames, ngakhale adapeza mwayi wochuluka kuposa Namibia, adalepherana ndi timuyo mumpikisano wolimbirana malo ku mpikisano…
Read More » -
Apolisi aphunzira kagwiridwe ka ntchito yawo
Polisi ya Nkhotakota yakhala yoyamba kuphunzitsidwa za momwe angagwirire ntchito yawo panthawi ya zipolowe komanso zionetsero. Maphunzirowa akudza poyang’anira chisankho…
Read More » -
‘BAMBO ATHOTHA MWANA’
Bambo wina m’mudzi mwa Nchada kwa T/A Nthondo ku Ntchisi amulamula kuti alipe mkazi wake ndi mwana wake wamkazi wa…
Read More » -
Woba chiponde ku Chiladzulu agwidwa
Bwalo la Chiradzulu layamba kuzenga mlandu Operations Manager wa kampane yolondera ya Global Communications Centre pomuganizira mlandu woba chiponde cha…
Read More » -
Mkulu wa kunyumba ya chisoni agwidwa ndi ziwalo
Abambo awiri omwe amagwira ntchito kunyumba yachisoni kuchipatala cha Kamuzu Central (KCH) akuzengedwa mlandu wodula maliseche a mtembo wa munthu…
Read More » -
‘Wogona’ ndi mwana wake pofuna mfumba agwidwa
Ndani adanena kuti chizimba cha mfumba ndi kugona ndi mwana wako? Izi zachitika ku Dedza komwe apolisi anjata bambo wa…
Read More » -
Amayi abisa katundu wa K16 000 mu panti
Ukathyali wakasololedwe wachitika pamalo omwetsera mafuta a Puma pa Wenela pomwe apolisi adanjata mkulu wina wa ku Zambia pomuganizira kuti…
Read More » -
Mpingo ukana mbusa womangidwa za zitupa
Mpingo wa Lord’s Chosen Charismatic Revival Ministries (LCCRM) wakana zomwe munthu wina wa ku Cameroon adauza nthambi yoona za anthu…
Read More » -
Maneb ikhutila ndi mayeso a sitandade 8
Bungwe loyendetsa mayeso la Malawi National Examinations Board (Maneb) lati lakhutira ndi mmene mayeso a Sitandade 8 ayambira. Mkulu wa…
Read More » -
Anthu a ku Likoma alirira Ilala
Anthu okhala pazilumba za Likoma ndi Chizumulu ati akulira ndipo moyo ukutentha chifukwa cha kusiya kuyenda kwa sitima ya Ilala.…
Read More » -
Bajeti iganizire mavuto a anthu
Ndondomeko ya chuma ndiyo chiyembekezo chachikulu tsopano chomwe chingachepetse mavuto omwe anthu akukumana nawo kaamba ka kukwera mitengo ya zinthu…
Read More » -
Apolisi anjatidwa pokhudzidwa ndi ophedwa pa zionetsero
Apolisi asanu ndi anayi adatengedwa m’sabatayi powaganizira kuti akudziwapo kanthu pa za ena amene adaphedwa pazionetsero za pa 20 Julaye…
Read More »