Chichewa

Zikavuta, nawo anthu amakoka ngolo

Listen to this article

ngolo

Ngolo imakokedwa ndi ng’ombe kapena abulu, koma pena zikavuta nawo anthu amakoka. Pachithunzipa, anyamatawa adakoka ngoloyi ng’ombe zitathawa. Nanga titani? Kodi ngoloyi ena satibera? Iwo adangoganiza zoyamba kukoka ulendo nayo pakhomo. Zikavuta zilibe dolo.—Bobby Kabango

Related Articles

Back to top button
Translate »